Mack zero khima

Mack zero khima Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Mack zero khima, Legal, Lilongwe.

Love πŸ’•
02/02/2024

Love πŸ’•

NGATI BODZA😭
19/01/2024

NGATI BODZA😭

 Mafumu a mtundu wa Chilhomwe ochokera m'maboma a Chiradzulu, Mulanje, Phalombe, Zomba, Blantyre komanso Thyolo adandaul...
19/01/2024



Mafumu a mtundu wa Chilhomwe ochokera m'maboma a Chiradzulu, Mulanje, Phalombe, Zomba, Blantyre komanso Thyolo adandaula za kulongedwa kwa Mfumu Kaduya kukhala Paramount wa mtundu wa Alhomwe.

Motsogozedwa ndi Senior Chief Nkhulambe a m'boma la Phalombe, Senior Chief Ndalama komanso Ngolongoliwa a m'boma la Thyolo, mafumuwa adandaula kuti phata la Alhomwe silikuyenera kutsogoleredwa ndi atsogoleri a mtundu wa Chinyanja, amene ali ndi Paramount Lundu ngati mtsogoleri wa mtundu wawo kale.

"Ndife okondwa kwambiri kuti a Pulezidenti awadzodza a Kaduya koma tikuyesetsa kusunga mtundu wathu wa Chilhomwe kuti usabalalike.

Ufumu wa a Kaduya siwachilomwe koma wachinyanja (Mang'anja). Sizingatheke boma kutenga muyao ndi kukamuzodza kukhala m'tsogoleri wa atumbuka," atero a Senior chief Nkhulambe.

Mafumuwa anachititsa msonkhano wa atolankhani ku bwalo la Mwene amamwene Chief Ngolongoliwa Ntunda Osema headquarters m'boma la Thyolo.

Wolemba Llywellenie Mpasa

Pa Khama pachema Maburundi Aishosha kumasuka mpaka kubaya Malawi pa Mimba ndi Mpeni.tikunena pano atseka ma shop ose ama...
19/01/2024

Pa Khama pachema Maburundi Aishosha kumasuka mpaka kubaya Malawi pa Mimba ndi Mpeni.tikunena pano atseka ma shop ose ama Burundi ndipo ose athawa.

16/01/2024

Simungasokoneze badman Ali moyo. 2024.

16/01/2024

ProVoice Lameck

Mfana uli bhoo
16/01/2024

Mfana uli bhoo

Eeeetu mamie wachabe πŸ˜‚πŸ™Œ
11/01/2024

Eeeetu mamie wachabe πŸ˜‚πŸ™Œ

Yamikani Fodya 14 years with Nyasa Big BulletsπŸ”” winning 7 Super LeagueπŸ”” 2 Presidential Cup πŸ”” 2 FDH Cup πŸ”” 2 Airtel Top 8 ...
07/01/2024

Yamikani Fodya 14 years with Nyasa Big Bullets
πŸ”” winning 7 Super League
πŸ”” 2 Presidential Cup
πŸ”” 2 FDH Cup
πŸ”” 2 Airtel Top 8
πŸ”” One Ibongetse Challenge cup
πŸ”” 2 Carsberg cup
, πŸ”” Charity Shield

With Malawi the Flames
πŸ”” COSAFA Plate Cup

Legend

07/01/2024

Muli ndi moyo wankhaza ngati Phwedo bwanjiπŸ”•

Address

Lilongwe

Telephone

+265991664686

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mack zero khima posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Practice

Send a message to Mack zero khima:

Share

Category