KuswaKuswa

KuswaKuswa Kwao kwachilungamo ndikuno.
(1)

23/04/2026

Kumaliwopa Mawa.

20/04/2026

Chimene chimamulimbitsa mtima mamuna wa chikafiri kuti akafusile nkazi wa chisilamu ndichakuti amaona kuti mkaziyo zachisilamu sakhala nazo serious ndipo sizingavute kuti azisiye.

Ichi mchifukwa chake akazi ozitsata za Deen samapangidwa approach ndima Kafir mwachisawawa.

Siraj Hussein.โœ๏ธ

14/04/2026

Eesh koma zambiri zikuchitikatu kunjaku bwanji koma
eeh ma sheikh this .
Eeh Nasheed yo angokuwamo mulibe mzazeru koma bolanso akanangoyetsemula.
Eeh Umbuli this n that ๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œ

palowatu mphepo yoipaa pamudzi pano zambiri sizuenda ai.

wapereka fatuwah iyi ndaani mwati??
12/04/2026

wapereka fatuwah iyi ndaani mwati??

Ana anganga kwereko
11/04/2026

Ana anganga kwereko

10/04/2026

Kwamene mumati masiku akanalipo six days mugwesabe kwasalatu 9/8 days kuti Shawwal athe muziwa koma

akutitu ngati simufuna kumvala bwinobwino hijab m***a kukangomujoiner Neba than kumationengera Chisilamu chokongolachi.m...
09/04/2026

akutitu ngati simufuna kumvala bwinobwino hijab m***a kukangomujoiner Neba than kumationengera Chisilamu chokongolachi.

mwamva abwande inuu

08/04/2026

Ofcoz munthu uja maphunziro adeen Ali nao koma ndi Content Creator amafuna azibeba nthawi zonse basi iyeyo koma Ambiri simuziwa ๐Ÿ˜€๐Ÿ˜€

mukachita mitu youmayo.

08/04/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Ish K M Millie, Sulaimana Rajabu Deulah, Angella Wayne Abilu, Aniz Maganga, Abada Lukia, Saidi Siyaya, Georgina Bless Biness, Abdullah Sheriff Mushe, Kellium Banda, Md Kasimu, Kassim Daud, Haneef Rabson, Ishmael M***a, Marupi Seriweke Marupi, Osman Lee Imraan, Hรฆลˆรฎฤ™ Phรชr Bรชthรฆ, SulaMuha SulaMuha, Monnirah James, Jacqueline James, Hafswa Raudha, Marryam Shaibu, RJ Noor Charles, Tuwen Manyamula, Gwaza Regoh Banda, Agness George

07/04/2026

kuchisilamuku zikanakhala kuti panikkah paja amafunsaso kuti alipo akuletsa tisanadalitse eeh ma artist Ambiri iiih I mean anthu Ambiri bwezi nthawi iyiyi akupenga misala ๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ

tiziyamika pokhala asilamu koma

Aaah  Neba Chipongwetu ichii  bwamba anzako awa ๐Ÿ˜‚
03/04/2026

Aaah Neba Chipongwetu ichii bwamba anzako awa ๐Ÿ˜‚

02/04/2026

Kodi ndekuti inuo mumapanga business yanji kapena anzanu amapanga business yanji post in comment box tiziwe nao ๐Ÿ˜Š Geni nkutsatsaa

Address

Blantyre

Telephone

+265881212646

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when KuswaKuswa posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share