Tikambe

Tikambe We talk the reality about people who oppresse others or mesmerize them by siding no one.

08/06/2016

Tikuona bwanji ndi ulamuliro wa Peter?

Anyamata awiri amangidwa ataba ndalama yothandizila ana amasiye ku zomba lero ku m'mawa
01/06/2016

Anyamata awiri amangidwa ataba ndalama yothandizila ana amasiye ku zomba lero ku m'mawa

ubatchala wandikwana
28/04/2016

ubatchala wandikwana

22/04/2016

Dziko la Malawi lalandira thandizo la ndalama zokwana $ 300 million kuchokela ku United nation kuti zithandize pa ntchito yolimbana ndi matenda a HIV ndi AIDs nzikoli,
President Mutharika wati ndalamayi ithandiza kugulila ma ARV ndi zakudya za anthu odwala matendawa mzipatala ndi m'midzi,

Dziko la Malawi ndi dziko limodzi lomwe lili pa tsogolo pa chiwelengero cha anthu odwala AID pa dziko lonse la pansi ndipo anthu okwana 745.000 amatenga matendawa pa week iliyonse.

Tiyeni tipemphe Mulungu achitepo kanthu ndi anthu tonse mu dziko la Malawi atichepetsele kufala kwa matendawa posatengela kusawuka kwa dziko lathu.

Pronouced by

21/04/2016

Dziko la Malawi lidali ndi mwayi otukuka pamene malemu Kamuzu Banda adali moyo koma ana ongoyamba kumene ndale anasokoneza ponamiza anthu kuti Kamuzu amapangazo zidali nkhaza kwa anthu pomwe zambiri mwa izo Kamuzu samazidziwa kamba koti panali ma meeting ena omwe Chakwamba ndi Tembo komanso Nduna zina za Kamuzu zimakambirana M'chichewa podziwa kuti Kamuzu samanva chichewa,
Ndipo akafika kwa anthu amawawuza kuti ndi Kamuzu yemwe amalamula zonsezi,
Kotero ndale zinalakwika Bakili Muluzi yemwe anali Secretary atatenga udindo wawu president kusiya Chakwamba ndi Tembo ali otsutsa Boma,

Lero atsogoleri komananso
Amipingo maso awo ali pofuna kulemera ndi ka ndalama kochepa komweko komwe mayiko akunja anzathu akupereka kuti amphawi azithandizika nako,
Koma dziwani kuti misonzi ya amphawi omwe akuzunzika mukusangalalawa siyizagwera pansi,
Mulungu azawayankha koma musamawakhomelele potseka zipata zawo zopezela chuna.

19/04/2016

Its so worrying to see that we have the same regime in the country which keeps on opressing and obliterating the moralities of Malawi residents, we know and believe that its only God-fearing leadership can benefit the majority and uplift the economic growth in the country rather than hipocrit,
We should also bear in mind that all politicians are greedy and selfish they care about poor when they want to stay in power, so for our good state we should say"
Let them take us to the river but they must not force us to drink water"
I hope you got my point.

15/04/2016

Peter Mutharika falls flat on his face story goes viral of the internet, kodi tiziti njala yatchuka pa Malawiyi ndi a president omwe ikuwakantha?

Dziko la Malawi likuvuta kutukuka kamba ka anthu a mzikoli amakakamira zinthu kuti zikhale mwachikale momwemo zikatukuka amadana nazo kumati Boma likubweretsa za kunja,
Kodi ndi njira iti yomwe mumafuna kuti dziko la Malawi lizatukukile?
President akapempha ma company akunja mumati akubweretsa satanic

Address

Balaka
319

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Tikambe posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share