REAL TAlk

REAL TAlk M I n d s e t c h a n g e

It's GCN on 🔥🔥
07/02/2026

It's GCN on 🔥🔥

07/02/2026
Mwaona zomwe amapanga ambuye tamuyeseni
08/09/2024

Mwaona zomwe amapanga ambuye tamuyeseni

20/04/2024

trap is a trap

14/10/2023

Mawa mmawa tili live pano page muyambe kuimva kukoma # fans

09/08/2023

Nde popephera muziti mulengi waphamvu zonse omwe mumadziwa ndisanachimwe ngankhale chomwe ndachimwa mukuzindikira mumadziwa ndiyendeseni mchifuniro chanu mudzina la yesu Christu yemwe anatenga machimo onse apadziko lapansi mutsinje wa yelodani ndikulilipira zonse pa mtanda panja Ife mkunkhala osachimwa mkupulumuka mwachisomo chake tikuti zikomo chifukwa ena aliku maula ndi kuma central hospital adziko lino amen tipatseni kufuna kwanu osati zilakolako zanthu

06/08/2023

Palibe oyera ndi yesu Christu yenkha zikumveka mmmmhuuuuuuu

06/08/2023

Koma ndee munaonjetu kkkkkkkkkk arsenal mumakwana kkkkkkkkk

06/08/2023

Komatu munagolakwatu? eyatu inu mukuona bwanji! kkkkkk happy Sunday to u all kkkkk😂😂😂😂😂

31/01/2022

new song

wanga

Apelepere NDi awa azitibweretsera Real life stories zomwe tiziphuzira zambiri mmoyo
14/01/2022

Apelepere NDi awa azitibweretsera

Real life stories zomwe tiziphuzira zambiri mmoyo

Address

Area 22 B
McHesi

Telephone

+265990486236

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when REAL TAlk posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category