02/10/2024
Malodza pa Malo okazinga mowa
Gabura ndi mzake Ndere ndi anyamata ochokera mu Dera la Dedza mfumu yayikulu Gwebede anyamatawa amakonda kumwa Mowa wa kabanga Iwo tsiku lina adapeza ganyu otipula kudimba kwa amfumu achatota.mfumuyi idawadalila popeza Iwo anali anyamata odzipereka pa ntchito atanadira malipilo awo,,,anyamatawa adaganiza zopita kwa mayi Natchezani kukadzipepesa ndi Bibida.Odi odi ,,,,Ea Aaah Kodi ndi Gabura kkkkk wandithamangitsatu nyamata bj osangolowa k*ti musambe nawo relo popeza ndi wamoto hhhhhhh mayi inu mpokoso likuveka lero ndilina ngat kuli chikisheni cha kundende,,,ayi ndi azanu akumwerera mkatimu ,,,lowani zikomo mayi anthu ,,,tilawe ,,,,aaaaaah uli bwino mowawu make thirani jomera uja ndimakukonda ndi mzangayu uja ,,,,, anyamatawa atatonyoka nawo mowa modzi mwa yiwo adati make?make?!!!!! Wee adayakha monyadira ogulisa mowa uja Gabura adati tayandikirani nanga anthu achite kumva nawo khalani ngat wakulu ,,,,,make tiwonetseni kokodzera................Gabura uk*ti chani? make musandichedwetse onetseni kokodzera amayi aja adanyamuka ndikumemeza anthu k*ti Gabura amafuna kuwagwililira ,,,,, anyamatawa adamenyedwa ngati akuba k*t thapsa ndipo adawatengera kubwalo la amfumu,,,mulandu unayamba Amfumu adati Gabura mayi Natchezani adadzadandaura k*ti umafuna kuwagwililira uk*tipo bj pakhaniyi ,,,,Gabura adati Zikomo mfumu yang mau anga si apatali chomwe naphedwera ine ndi mau ak*ti amayiwa andiwonetse kokodzera ndipo pathawiyi mk*ti ndikufuna andilonzere nyumba yokataya madzi km adandiganizira ngat wachipongwe zkm kumpando..guru lonse linangoti haaaaaaaaa kuwawowoza mayi Natchezani ,,