21/10/2024
Nthawi yomwe ndidali mwana makolo zikawavuta kumbali yachakudya cha mamawa samkakwanitsa kuti tizidya masiku onse koma ine ndimkawakwiyila
Nthawi zina amabweletsaso ndiwo zosapeleka chikoka ndimkawateroso.
Koma Pano ndakulano ndipamene ndadziwa kuti nthawi ija makolo amkabweletsa chakudya pakhomo siyinali ntchito yamasewera π.
Abale kusaka sikophweka tikuyenela tiziwapatsa ulemu daily makolo athu ππ₯°β