Deep Precious Erick

Deep Precious Erick Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Deep Precious Erick, Legal, Area 25b, Lilongwe.

Ambuye mulipo kumwambako tonthozani kulira Kwa achibare ndi ana awo komaso makolo agulu la anthu atisiya pangozi iyi yak...
22/08/2024

Ambuye mulipo kumwambako tonthozani kulira Kwa achibare ndi ana awo komaso makolo agulu la anthu atisiya pangozi iyi yakupsa Kwa galimoto kukasungu😭😭😭😭😭😭😭R I P

Mukundikumbukira koma inee???⤴️
06/04/2024

Mukundikumbukira koma inee???⤴️

20/12/2023

This version of Facebook uses less data and works in all network conditions.

20/12/2023

Kodi mwava chimene chapangisa kuti papa ayankhure izi kapena mungova kuti zilichomcho chonde nkharani osamalisisa NGATI MUKUFUNA KUVA ZAMBIRI PANGANI FOLLOW OR LIKE THIS PAGE 📄

18/12/2023

SIMBI
Simbi ndimunthu wandalama zake zochuluka kwambiri ndipo munthu amene wamupangira zomusangalasa samachedwa kumunthokoza pomupasa ndalama kotero simbi ndimmodzi mwa anthu andalama zawo.

ANAZIPEZA MOTANI
Mkulu alimeneyi kuchokera pachiyambi anali mmisiri wazomangamanga kotero amagwira timaganyu ngati mmene amapangiraso amisiri ena kotero simbi anatengedwa ndi foman wina kuti akagwire naye ntchito pakampani ina m,boma la Blantyre mchaka cha 1967 ndipo simbi anapita mokondwera atangogwira kwamasiku wochepa forman wake uja anayamba kuva kuwawa mnthupi kotero anatsazika ndikubwerera kunyumba ndipo formaniyo anawatsimikizira mabwana akewo kuti asankhare ndi nkhawa ntchitoyo igwilika moyenera ndipo pamapeto ake zinapezeka kuti simbi wagwira ntchitoyo kuposaso forman wake uja
ZINANKHALA BWANJI
zitatero simbi anamuuza kuti ankhare wowonelera azake wose pamalopo ndipo simbi samamuyiwara forman wake amatumiza ndalama moyenera akalandira patapita ma week atatu zachisoni forman wake uja anamwalira ndipo mwambo wamaliro utantha simbi anawapempha abawana ake kuti akufuna ayime kaye kugwira ntchitoyo ponkhara ndimalongaliro aanthu kuti angamuganizire morakwika koma bwana uja anakana kuti zitero ndipo simbi anangonkhara masiku okwana 5 ndikupitaso kuntchitoko atafika anamuuza kuti ntchito yako sugwiliraso pano tikukutumiza Ku Zambia ukanthandizire kumanga nyumba za boma ndipo anamupasa njinga yamoto komaso Dalaivara womuyendesa.
ATAFIKA ZAMBIA
simbi chifukwa chamagwilidwe ake antchito azungu Aku Zambia anamutumiza Ku south Africa.ndipamene simbi anazindikira kuti iyeyo tsopano ndibwana wamkulu koma ndipo simbi atafika mmene amkafunira minthawi imene asanayiphure anakwanilidwa ndipo anganiza zosiya ntchito koma bwana anamunyengekera pomuuza kuti akufuna atsegure kampani koma inkhare yawiliwo kotero simbi sanazwngereze koma kuvomera kuchokera nthawi imeneyo simbi ndimunthu wandalama
KODI SIMBI SANAKWATILEPO NDIPO ALIBE MWANA CHIFUKWA CHANI pangani follow pageyi ndikupanga like

Address

Area 25b
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Deep Precious Erick posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category